Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace asungeni, aciteni; pakuti ici ndi nzeru zanu ndi cidziwitso canu pamaso pa mitundu ya anthu akumva malemba ndi kuti, Ndithu mtundu waukuru uwu, ndiwo anthu anzeru ndi akuzindikira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:6 nkhani