Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 4:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena kodi anayesa Mulungu kumuka ndi kudzitengera mtundu mwa mtundu wina wa anthu, ndi mayesero, ndi zizindikilo, ndi zozizwa, ndi nkhondo, ndi mwa dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mwa zoopsa zazikuru, monga mwa zonse Yehova Mulungu wanu anakucitirani m'Aigupto pamaso panu?

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:34 nkhani