Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mutakabala ana, ndi zidzukulu, ndipo mutakakhala nthawi yaikuru m'dzikomo, ndi kudziipsa, ndi kupanga fano losema, m'cifaniziro ca kanthu kali konse, ndi kucita coipa pamaso pa Yehova, kuutsa mkwiyo wace:

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:25 nkhani