Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 33:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wodala iwe, Israyeli;Akunga iwe ndani, mtundu wa anthu opulumutsidwa ndi Yehova,Ndiye cikopa ca thandizo lako,Iye amene akhala lupanga la ukulu wako!Ndi adani ako adzakugonjera; Ndipo udzaponda pa misanje yao.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33

Onani Deuteronomo 33:29 nkhani