Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 33:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Ndipo za Yosefe anati,Yehova adalitse dziko lace;Ndi zinthu zofunikatu za m'mwamba, ndi mame,Ndi madzi okhala pansipo;

14. Ndi zipatso zofunikatu za dzuwa,Ndi zomera zofunikatu za mwezi,

15. Ndi zinthu zoposa za mapiri akale,Ndi zinthu zofunikatu za zitunda zosatha,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33