Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 33:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzaphunzitsa Yakobo maweruzo anu,Ndi Israyeli cilamulo canu;Adzaika cofukiza pamaso panu,Ndi nsembe yopsereza yamphumphu pa guwa la nsembe lanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33

Onani Deuteronomo 33:10 nkhani