Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 32:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kubwezera cilango nkwanga, kubwezera komwe,Pa nyengo ya kuterereka phazi lao;Pakuti tsiku la tsoka lao layandika,Ndi zinthu zowakonzeratu zifulomira kudza.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32

Onani Deuteronomo 32:35 nkhani