Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndidzawapsera mtima tsiku ilo, ndipo ndidzawataya, ndi kuwabisira nkhope yanga, ndipo adzathedwa, ndi zoipa ndi zobvuta zambiri zidzawafikira; kotero kuti adzati tsiku lija, Sizitifikira kodi zoipa izi popeza Mulungu wathu sakhala pakati pa ife?

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:17 nkhani