Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Taona, ayandikira masiku ako akuti uyenera kufa; kaitane Yoswa, nimuoneke m'cihema cokomanako, kuti ndimlangize. Namuka Mose ndi Yoswa, naoneka m'cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:14 nkhani