Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anawauza, ndi kuti, Pakutha pace pa zaka zisanu ndi ziwiri, pa nyengo yoikika ya m'caka cakulekerera, pa madyerero a misasa;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:10 nkhani