Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza ndikuuzani lero kukonda Yehova Mulungu wanu, kuyenda m'njira zace, ndi kusunga malamulo ace ndi malemba ace ndi maweruzo ace, kuti mukakhale ndi moyo ndi kucuruka, ndi kuti Yehova Mulungu wanu akakudalitseni m'dziko limene mulowako kulilandira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:16 nkhani