Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muja tinalanda midzi yace yonse; kunalibe mudzi sitinaulanda m'manja mwao, midzi makumi asanu ndi limodzi, dera lonse la Arigobi, dziko la Ogi m'Basana.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3

Onani Deuteronomo 3:4 nkhani