Deuteronomo 3:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma langiza Yoswa, dioloketu numlimbitse mtima, ndi kumkhwimitsa, pakuti adzaoloka pamaso pa anthu awa