Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambuye Yehova, mwayamba Inu kuonetsera mtumiki wanu ukulu wanu, ndi dzanja lanu lamphamvu; pakuti Mulungu ndani m'mwamba kapena pa dziko lapansi wakucita monga mwa nchito zanu, ndi monga mwa mphamvu zanu?

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3

Onani Deuteronomo 3:24 nkhani