Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzamsiyanitsa ndi mafuko onse a Israyeli ndi kumcitira coipa, monga mwa matemberero onse a cipangano colembedwa m'buku ili la cilamulo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:21 nkhani