Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 29:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi mau a cipangano cimene Yehova analamulira Mose acicite ndi ana a Israyeli m'dziko la Moabu, pamodzi ndi cipanganoco anacita nao m'Horebe.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:1 nkhani