Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 28:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwamuna wololopoka nkhongono ndi wanyonga pakati pa inu diso lace lidzaipira mbale wace, ndi mkazi wa pa mtima wace, ndi ana ace otsalira;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:54 nkhani