Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 28:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakuzingani m'midzi mwanu monse, kufikira adagwa malinga anu atali ndi olimba, amene munawakhulupirira, m'dziko lanu lonse; inde, adzakuzingani m'midzi mwanu monse, m'dziko lanu lonse limene Yehova Mulungu wanu akupatsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:52 nkhani