Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 28:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kudzali, mukapanda kumvera mau a Yehova Mulungu wanu, kusamalira kucita malamulo ace onse ndi malemba ace amene ndikuuzani lero, kuti matemberero awa onse adzakugwerani ndi kukupezani,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:15 nkhani