Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 27:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Wotembereredwa iye wakukantha mnansi wace m'tseri. Ndi anthu onse anene, Amen.

25. Wotembereredwa iye wakulandira camwazi cakuti akanthe munthu wosacimwa. Ndi anthu onse anene, Amen.

26. Wotembereredwa iye wosabvomereza mau a cilamulo ici kuwacita. Ndi anthu onse anene, Amen.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 27