Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 26:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muyankhe ndi kuti pamaso pa Yehova Mulungu wanu, Kholo langa ndiye M-aramu wakuti atayike, natsika kumka ku Aigupto, nagoneragonera komweko ali nao anthu pang'ono, nasandukako mtundu waukuru, wamphamvu, ndi wocuruka anthu ace;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26

Onani Deuteronomo 26:5 nkhani