Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mkazi wa mbale wace azimyandikiza pamaso pa akuru, nacotse nsapato yace ku ph zi la mwamunayo, ndi kumthira malobvu pankhope pace, ndi kumyankha ndi kuti, Atere naye mwamuna wosamanga nyumba ya mbale wace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:9 nkhani