Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati mwamunayo safuna kutenga mkazi wa mbale wace, mkazi wa mbale waceyo azikwera kumka kucipata, kwa akuru, ndi kuti, Mbale wa mwamuna wanga akana kuutsira mbale wace dzina m'Israyeli; safuna kundicitira ine zoyenera mbale wa mwamuna.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:7 nkhani