Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 25:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abale akakhala pamodzi, nafa wina wa iwowa, wopanda mwana wamwamuna, mkazi wa wafayo asakwatibwe ndi mlendo wakunja; mbale wa mwamuna wace alowane naye, namtenge akhale mkazi wace, namcitire zoyenera mbale wa mwamuna wace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:5 nkhani