Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 25:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, pamene Yehova Mulungu wanu atakupumulitsirani adani anu onse ozungulira, m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colowa canu canu, kuti muzifafaniza cikumbutso ca Amaleki pansi pa thambo; musamaiwala.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:19 nkhani