Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 24:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mutasenga dzinthuzanu m'munda mwanu, ndipo mwaiwala mtolo m'mundamo, musabwererako kuutenga; ukhale wa mlendo, wa mwana wamasiye, ndi wa mkazi wamasiye; kuti Yehova Mulungu wanu akudalitseni m'nchito zonse za manja anu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:19 nkhani