Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 24:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa tsiku lace muzimpatsa kulipira kwace, lisalowepo dzuwa; pakuti ndiye waumphawi, ndi mtima wace ukhumba uku; kuti angakulirireni kwa Yehova, ndipo kukukhaireni cimo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:15 nkhani