Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza Yehova Mulungu wanu ayenda pakati pa cigono canu, kukupulumutsani ndi kupereka adani anu pamaso panu; cifukwa cace cigono canu cikhale copatulika; kuti angaone kanthu kodetsa mwa inu, ndi kukupotolokerani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23

Onani Deuteronomo 23:14 nkhani