Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 22:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Musamabzala mbeu zosiyana m'munda wanu wamphesa, kuti zingaipsidwe mbeu zonse udazibzala, ndi zipatso za munda wamphesa zomwe.

10. Musamalima ndi buru ndi ng'ombe zikoke pamodzi.

11. Musamabvala nsaru yosokonezeka yaubweya pamodzi ndi thonje.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 22