Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 22:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukacipeza cisa ca mbalame panjira, mumtengo kapena panthaka pansi, muli ana kapena mazira, ndi mace alikuumatira ana kapena mazira, musamatenga mace pamodzi ndi ana;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 22

Onani Deuteronomo 22:6 nkhani