Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 22:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

muziwaturutsa onse awiri kumka nao ku cipata ca mudzi uwo, ndi kuwaponya miyala kuti afe; namwaliyo popeza sanapfuula angakhale anali m'mudzi; ndi mwamuna popeza anacepetsa mkazi wa mnansi wace; cotero muzicotsa coipaco pakati panu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 22

Onani Deuteronomo 22:24 nkhani