Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 21:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ansembe, ana a Levi, ayandikize; pakuti Yehova Mulungu wanu anasankha iwo kumtumikira ndi kudalitsa m'dzina la Yehova; ndipo kutengana konse ndi kupandana konse kukonzeke monga mwa mau awa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21

Onani Deuteronomo 21:5 nkhani