Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 20:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akapitao anenenso kwa anthu, ndi kuti, Munthuyo ndani wakucita mantha ndi wofumuka mtima? amuke nabwerere kunyumba kwace, ingasungunuke mitima ya abale ace monga mtima wace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 20

Onani Deuteronomo 20:8 nkhani