Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 20:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene muturuka pa mdani wanu kunkhondo, ndi kuona akavalo ndi magareta ndi anthu akucurukira inu, musawaopa; popeza Yehova Mulungu wanu, amene anakukwezani kukuturutsani m'dziko la Aigupto, ali ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 20

Onani Deuteronomo 20:1 nkhani