Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo tinatembenuka ndi kudzera njira ya cipululu ca Moabu. Ndipo Yehova anati kwa ine, Usabvuta Moabu, kapena kuutsana naye nkhondo; popeza sindidzakupatsako dziko lace likhale lako lako; pakuti ndinapatsa ana a Loti Ari likhale lao lao.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:9 nkhani