Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova Mulungu wanu anakudalitsani mu nchito zonse za manja anu; anadziwa kuyenda kwanu m'cipululu ici cacikuru; zaka izi makumi anai Yehova Mulungu wanu anakhala ndi inu; simunasowa kanthu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:7 nkhani