Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira ku Aroeri, ndiko kumphepete kwa mtsinje wa Arinoni, ndi ku mudzi wokhala kumtsinje kufikira ku Gileadi, kunalibe mudzi wakutitalikira malinga ace; Yehova Mulungu wathu anapereka yonse pamaso pathu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:36 nkhani