Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ukadzasunga lamulo ili lonse kulicita, limene ndikuuzani lero lino, kukonda Yehova Mulungu wanu, ndi kuyenda m'njira zace masiku onse; pamenepo mudzionjezere midzi itatu yina pamodzi ndi itatu iyi;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:9 nkhani