Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 18:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Kapena wotsirika, kapena wobwebweta, kapena wopenduza, kapena wofunsira akufa.

12. Popeza ali yense wakucita izi Yehova anyansidwa naye; ndipo cifukwa ca zonyansa izi Yehova Mulungu wanu awapitikitsa pamaso panu.

13. Mukhale angwiro ndi Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18