Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ansembe Alevi, pfuko lonse la Levi, alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi Israyeli; azizidya nsembe zamoto za Yehova, ndi colowa cace,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:1 nkhani