Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamaphera Yehova Mulungu wanu nsembe ya ng'ombe, kapena nkhosa, yokhala naco cirema, kapena ciri conse coipa; pakuti cinyansira Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17

Onani Deuteronomo 17:1 nkhani