Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma pamalo pamene Yehova Mulungu wanu adzasankha kukhalitsapo dzina lace, pamenepo muphere nsembe ya Paskha, madzulo, polowa dzuwa, nyengo ya kuturuka inu m'Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:6 nkhani