Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzicenjerani, mungakhale mau opanda pace mumtima mwanu, ndi kuti, Cayandika caka cacisanu ndi ciwiri, caka ca cilekerero; ndipo diso lanu lingaipire mbale wanu waumphawi, osampatsa kanthu; ndipo iye angalirire inu kwa Yehova; ndipo mwa inu mungakhale cimo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15

Onani Deuteronomo 15:9 nkhani