Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo abwere Mlevi, popeza alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi inu, ndi mlendo, ndi ana amasiye, ndi mkazi wamasiye, okhala m'mudzi mwanu, nadye nakhute; kuti Yehova Mulungu wanu akakudalitseni mu nchito zonse za dzanja lanu muzicitazi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14

Onani Deuteronomo 14:29 nkhani