Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mugule ndi ndaramazo ciri conse moyo wanu ukhumba, ng'ombe kapena nkhosa, kapena vinyo, kapena cakumwa colimba, kapena ciri conse moyo wanu ukufunsani; nimudye pomwepo pamaso pa Yehova Mulungu wanu, ndi kukondwera, inu ndi a pabanja panu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14

Onani Deuteronomo 14:26 nkhani