Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:11-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Mbalame zosadetsazonse muyenera kumadya.

12. Koma izi ndi zimene simuyenera kumadya: mphungu, ndi nkhwazi, ndi cikambi,

13. ndi kamtema, ndi mphamba, ndi muimba monga mwa mtundu wace;

14. ndi khungubwe ali yense monga mwa mtundu wace;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14