Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pasamamatire padzanja panu kanthu ka cinthu coti cionongeke; kuti Yehova a aleke mkwiyo wacewaukali, nakucitireni cifundo, ndi kukumverani nsoni, ndi kukucurukitsani monga analumbirira makolo anu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:17 nkhani