Amuna ena opanda pace anaturuka pakati pa inu, naceta okhala m'mudzi mwao, ndi kuti, Timuke titumikire milungu yina, imene simunaidziwa;