Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

dzicenjerani nokha mungakodwe ndi kuwatsata, ataonongeka pamaso panu; ndi kuti mungafunsire milungu yao, ndi kuti, Amitundu awa atumikira milungu yao bwanji? ndicite momwemo inenso.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:30 nkhani