Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi cimene anacitira Datani ndi Abiramu, ana a Eliabu, mwana wa Rubeni; muja nthaka inatsegula pakamwa pace, ndi kuwameza iwo, ndi mabanja ao, ndi mahema ao, ndi za moyo zonse zakuwatsata pakati pa Israyeli wonse.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 11

Onani Deuteronomo 11:6 nkhani